Kal-El Music – Bwenzi Nditabwelera (Prod by Dr Udio)Kal-El Music – Bwenzi Nditabwelera (Prod by Dr Udio)
Lyrics Ine ndikhumba, Mbuye YesuMudzakhale pompo mkamadzafaNdikamasimba za imfa yangaAbwenzi ambiri samakondwaKoma ndithu tonsefe tidzafaNgati si mawa mwina mkujaIne nditi pa maliro angaMsadzachulutse kundiyamika Nzimu wanga udzakondwa, (powona kuti)Odwala athandizidwa