


Lucius Banda_Mzimu wa Soldier spirit of a soldier
Lyrics Ine ndikhumba, Mbuye YesuMudzakhale pompo mkamadzafaNdikamasimba za imfa yangaAbwenzi ambiri samakondwaKoma ndithu tonsefe tidzafaNgati si mawa mwina mkujaIne nditi pa maliro angaMsadzachulutse kundiyamika Nzimu wanga udzakondwa, (powona kuti)Odwala athandizidwa (mwachangu ndi chikondi)Pa anthenda aweluzidwa (asanamangidwe)Wana amayi amasiye (zawo alandire) Nzimu wa Soldier udzagonaNzimu wa Soldier udzagonaWana amphawi ndi wolemera aphunzire zimodziNgakhale wolemera akalakwa amangidweOlumara…



