🔥 Nkhani yabwino kwa achinyamata onse ozungulira Blantyre!
KWAKONZEDWA MIC BATTLE COMPETITION — Yabweranso Mwaukulu komanso Mokweza Kwambiri! 🎤🔥
🎶 Mphoto zonse: MK200,000
💪 Amuna: K100,000 | 👑 Akazi: K100,000
✨ Inu uuwuutu ndi mwayi wanu oti muonetse luso lanu, muime pa stage, ndikutenga ndalama imeneyi!
🔥 Kodi uli ndi mphamvu zotenga mic ndi kuwunikira luso lako?
📢 Kulembetsa kwatseguka — K5000 yokha!
Lola mawu ako amveke, ndipo uwonetse kuti Blantyre ili ndi talente yeniyeni! 🌟🎶
MicBattle #RedAppleVisuals #TalentShow #MalawiMusic #KachereKc @highlight
📞 Kuti mudziwe zambiri, tiyankhuleni ku RED APPLE VISUALS!
👉 Auzeni anzanuwo — nawoso auze anzawo zakhaniyi! 🔥🎤💯
REGISTER NOW!! +265 882576282