Kell Kay’s Upcoming Album

IMG 9177

Malawian music fans, get ready! Kell Kay has announced the release of his third album,“Ndabwera Ndi Nkhani (Vol. 2)”, set to drop next week. Unfortunately,details about the album’s tracklist and features are scarce. Fans are eagerly awaiting the release,excited to see what Kell Kay has in store. Stay tuned for more updates!”

KWAKONZEDWA MIC BATTLE COMPETITION (Nkhani yabwino kwa achinyamata onse ozungulira Blantyre!)

PHOTO 2025 10 09 10 12 41

🔥 Nkhani yabwino kwa achinyamata onse ozungulira Blantyre!KWAKONZEDWA MIC BATTLE COMPETITION — Yabweranso Mwaukulu komanso Mokweza Kwambiri! 🎤🔥 🎶 Mphoto zonse: MK200,000💪 Amuna: K100,000 | 👑 Akazi: K100,000 ✨ Inu uuwuutu ndi mwayi wanu oti muonetse luso lanu, muime pa stage, ndikutenga ndalama imeneyi!🔥 Kodi uli ndi mphamvu zotenga mic ndi kuwunikira luso lako? 📢 … Read more